Mawu ku mpingo.

<< m'mbuyomu

lotsatira >>

  Wamoyo Mawu mndandanda.

Mawu ku mpingo.

Werengani akaunti yonse mu...
  Khristu ndi chinsinsi cha Mulungu woululidwa.


William Branham.

Zikondanani wina ndi mzake, pamwamba pa chirichonse. Kondanani wina ndi mzake. Musati... Ziribe kanthu zimenemdierekezi aziyesera kuti anene! Tsopano ndinu nonse gululimodzi lokoma lalikulu kwambiri tsopano, koma kumbukiranichenjezo langa, mwaona, Satana salola izo kuti zikhalemwanjira imeneyo.

Ayi, bwana. Iye adzawombera chirichonse, ngati iye angati amubweretse wina umo kuti amupangechandamale chake. Iye adzabweretsa wotsutsa wina kapenawosakhulupirira umo, ndi kumukhazika iye pansi, ndikumupangitsa iye kuti aziyanjana ndi inu pansi pakachetechete ndi zinthu, ndiyeno iye adzamuwombera munthuameneyo ndi mtundu wina wa chinthu chachiphe, ndipo iyeadzayamba kudutsa mu mpingo ndi izo. Inu musati mutengembali ndi izo. Inu musati mukhale ndi chinthu chochita ndichina chirichonse. Inu mukhalebe okonda ndi okoma ndiachifundo kwa wina ndi mzake. Muzimupempherera munthuameneyo, kuti iye adzapulumutsidwe nayenso, kapena mkaziameneyo, kapena yense yemwe iye ali, muziwapemphereraiwo. Ndipo mamatiranani wina ndi mzake. Ndipo khalani ndi m'busa wanu. Mwaona, iye ndi m'busa, ndipo inu muzimupatsa iye ulemu. Iye adzakutsogolerani inumopyola, ndipo, chifukwa iye ndi wodzozedwa ndi Mulungukuti achite chomwecho.

Tsopano kodi inu mukukumbukira zimenezo? [Osonkhanaati, “Ameni.”- Mkonzi.] Mdani adzabwera. Ndipo pamene iyeatero, muzingomamatirana mofupikirana limodzi chotero. Ndipo yemwe mdierekezi akumugwiritsa ntchito ngati mdanimwina atuluka kapena abwera mkati ndi kukhala mmodzi wainu. Ndizo zonse. Musati konse muzipanga timagulu pakati pa inu, kapena kuyankhula ndi kudzipanga nokha mwakamtundu. Ifendife amodzi.

Ine sindikanati, “Dzanja lamanzere, ine_inendalusa pa iwe, ine ndikuchotsapo iwe chifukwa iwe sindiwedzanja lamanja.” Iye ndi dzanja langa lamanzere. Inendikufuna iye kuti akhale pamenepo. Ngakhale nsongayaing'ono ya chala changa, ine ndikufuna kuti ikhale apopomwe, gawo laling'ono lirilonse la thupi langa likhale apopomwe. Ndipo Mulungu akutifuna ife, monga thupi laokhulupirira, kuti tikhale ndendende kumene ndi wina ndimzake, kumene pa wina ndi mzake.

Ndipo tsopano inu muli nawo matepi pa izo. Inu muli nawomatepi pa zimene ife timakhulupirira. Inu muli nawo matepipa khalidwe mu mpingo, momwe ife timadzikhalitsira mumpingo wa Mulungu, momwe ife tiyenera kumabwerera munopalimodzi ndi kukhala limodzi mu malo Ammwambamwamba. Musati muzikhala kunyumba. Ngati Mulungu ali mu mtimawanu, inu simungakhoze konse kuyembekezera zitseko izo kutizitsegulidwe uko, kuti mulowe muno kudzayanjana ndi abaleanu. Ngati inu simutero, simumverera mwanjira imeneyo, ndiye ine ndikukuuzani inu, ndi nthawi yoti muyenerakumapemphera. Chifukwa, ife tiri mu masiku otsiriza, pamene Baibulolinatikweza... kapena linatilimbikitsa ife kuti, “Mochuluka kwambiri pamene ife tikuwona tsiku ilolikuyandikira,” kuti tizikondana wina ndi mzake ndi chikondicha Chikhristu ndi chikondi Chaumulungu, “kutitizidzisonkhanitsa tokha palimodzi mu maloAmmwambamwamba ndi Khristu Yesu,” ndikukondana wina ndi mzake. “Potere anthu onse adzadziwakuti inu ndinu ophunzira Anga, pamene inu muli nachochikondi wina kwa mzake.” Ndiko kulondola. Khalani kumenelimodzi.

Ngati m'bale, inu mukuganiza kuti iye akulakwitsapang'ono, kapena mlongo, itini, “Ambuye, musati mundiroleine ndikhale nao konse muzu wa chowawa ukutumphukirammwamba, chifukwa iwo... iwo umukhudza iye, ndipo iwoungachotse Khristu kumene kumuchotsa mmoyo wanga.” Chiphe cha asidi icho cha kuipamtima, ndi nsanje, ndi udani, zimene ziti zingouchotsa Mzimu Woyera apo pomwekuchokera mwa inu. Izo zingamuthamangitse Iye kumuchotsapa Kachisi pano. Izo zingaphe Mzimu wa Mulungu, kapena kuwuthamangitsa Iwo kuuchotsa pano, kumupweteka m'busawanu. Izo zingachite chirichonse. Mukuona? Musati inumuzichita zimenezo. Inu mungomamatirana moyandikirana limodzi mochulukachomwecho. Muzikoka... Mutenge lamba, monga m'baleanachitira umboni, mtumiki pano usiku wina, zakukhala ndichomangila, anaziwona izo mu masomphenya. Basi... Ameneamamangira pa zida zonse za Mulungu. Kumangokoka pa iye, kumangitsa, kusunthira uko pafupi ndi wina ndi mzake. Kukondana wina ndi mzake, mulimonse. Kuyankhulamwabwino za wina ndi mzake, kunena zinthu zabwino za winandi mzake, ndiyeno Mulungu adzakudalitsani inu.

Werengani akaunti yonse mu...
  Khristu ndi chinsinsi cha Mulungu woululidwa.


  Lemba linena...

Dzuka, wala, pakuti kuwala kwako kwafika, ndipo ulemerero wa Yehova wakuwalira.

Taona, mdima waphimba dziko lapansi ndipo mdima wandiweyani wagwa pa anthu a mitundu ina, koma Yehova adzakuwalira iwe, ndipo ulemerero wake udzaoneka pa iwe.

Yesaya 60:1-2


Dinani pa chithunzi tsitsani chachikulu chithunzi kapena PDF.


Acts of the Prophet

(PDF Chingerezi)
 

Khristu ndi chinsinsi
cha Mulungu
woululidwa.
(PDF)

Kale...

Pambuyo...

Mbiri ya moyo wanga.

(PDF)

Momwe ngelo anadzera
kwa ine olalikidwa ndi.

(PDF)