Mwalandiridwa webusaiti utumiki a BNL.
Quote...
Tsopano, ku mutu wanga, kuti ndiswere mmbuyo pa phunziro limene ine ndikufuna kuti ndilitenge pamenepo, mawu anai. Tiyeni tifotokoze, “kumeneko.” “Kumeneko,” mzinda woyera kwambiri mu dziko, Yerusalemu. “Kumeneko,” mzinda wachipembedzo kwambiri mu dziko. Kumeneko, “iwo,” anthu achipembedzo kwambiri mu dziko, pa phwando la chipembedzo, phwando la Paskha. “Kumeneko,” malo achipembedzo kwambiri, mzinda wachipembedzo kwambiri, bungwe lalikulukulu mwa mabungwe onse, mutu wa zinthu zonse, kumeneko, “iwo,” anthu achipembedzo kwambiri pa dziko lonse, anali atasonkhana kuchokera konsekonse mu dziko. Iwo “anamupachika,” imfa yochititsa manyazi kwambiri yomwe ikadakhalapo, kumupha, munthu akanakhoza kuphedwa nayo; wamaliseche, atamuvula zovala kuzichotsa pa Iye. “Iye ananyoza chitonzo.” Mtanda uli nako kasanza katakulungidwa pa Iye; koma iwo anamuvula zovala Zake. Yochititsa manyazi kwambiri...
“Kumeneko,” (mzinda wawukulukulu wachipembedzo,) “iwo,” (anthu achipembedzo kwambiri,) “anamupachika,” (imfa yamanyazi kwambiri,) “Iye,” (Munthu wofunika kwambiri.)William Branham - Chitsutso 63-0707M P33 (PDF)
Quote kuchokera
Fyuluta ya munthu woganiza.