Chisindikizo Chachisanu ndi Chiwiri.

<< m'mbuyomu

lotsatira >>

  Mndandanda Zisindikizo-Zisanu ndi ziwiri.

Munali chete m'mwamba.


William Branham.

Werengani akaunti yonse mu...
Chisindikizo Chachisanu ndi Chiwiri.

Ndipo tsopano ife tikupeza izo kuti, nafenso, ife. Ambuye atilore ife titenge Lemba, Lemba Loyera, chimene Yesu anati chikanadzachitika. Ndipo ife tikanachipeza bwanji icho konse? Ndipo apa, chikubwerapo ndi kuwulula, ndi kuchibweretsa icho chimodzimodzi basi. ulaliki wake pamenepo, poyankha izo, kukubweretsa chimodzimodzi pa nsonga, zisanu ndi chimodzi za Zisindikizo, koma lye anadumpha chachisanu ndi chiwiri. Ndiye pamene Zisindikizo zinatsegulidwa, Mulungu, zindikirani apa, lye anadumpha kuwulula ngakhale chiphiphiritso chirichonse cha chachisanu ndi chiwiri lcho. Mukuwona? Ndicho chinsinsi changwiro ndi Mulungu. Zindikirani. Tsopano ife tiwerenga mu Baibulo, mu chisindikizo chachisanu ndi chiwiri. chimene chikupezeka mu Chivumbulutso, mutu wa 8.

Ndipo pamene iye anali atatsegula chisindikizo chachisanu ndi chiwiri, munali chete m'mwamba pafupi kadanga ka theka la ora.
[Ndizokhazo zomwe ife tiri nazo pa icho]

Tsopano, palibe aliyense wa ife akudziwa. Koma, ine ndiri- ine ndikuwuzani inu, mu langa-vumbulutso langa la lcho. Ndipo, tsopano, ine sindiri woyandikira kuti ndikhale wotentheka. Ngati ine ndiri, ine ndiri wosadziwa za icho, mwawona. lne ndiri.ine sindinapatsidwe zotero monga zikhumbo zoyipa zomangopitirira ndi zinthu zongolingalira. lne ndalankhula zinthu zina, mwina zinali ngati zachirendo kwa anthu ena. Koma pamene Mulungu abwera pozungulira, kuseri kwa lcho, ndi kuchitsimikizira lcho ndi kunena kuti lcho chiri chowonadi, ndiye ndiwo Mawu a Mulungu. Mukuwona? lzo zikhoza kuwoneka zachirendo, mwanjira iyo. Mukuwona. Ndipo tsopano, motsimikiza monga ine ndikuyimira mu nsanja usiku uno, ine ndinali nalo vumbulutso lomwe linawulula. Chiri mu chikhalidwe chofutukuka patatu. lzo ine ndilankhula kwa inu, mwa kuthandiza kwa Mulungu, za kufutukuka kwa lcho. Ndiyeno inu.Tiyeni tidutse pa izo, poyamba. Apa pali vumbulutso, kuti ndiyambe zomwe ine ndikufuna kukuwuzani inu, chomwe lcho chiri. Chimene chikuchitika, chiri chakuti.Mabingu Asanu ndi awiri awo omwe iye anawamva akugunda, ndipo analetsedwa kuti Alembe... ndicho chimene chinsinsi chiri, chagona kuseri kwa Mabingu Asanu ndi awiri otsatana awo akulindimuka.

Tsopano, chifukwa? Tiyeni ife titsimikizire izo. Chifukwa? lzo ziri chinsinsi chimene palibe mmodzi akudziwa za icho. Yohane analetsedwa kulemba za lcho, ngakhale- ngakhale kulemba chophiphiritsa cha lcho. Chifukwa? lchi ndi chifukwa chomwe uko kunalibe chochitika Mmwamba: icho chikhoza kupereka chinsinsi. Kodi mukuziwona izo tsopano? Ngati lcho chiri chachikulu, lcho chiyenera kuphatikizidwa, chifukwa lcho chiyenera kuchitika. Koma pamene Mabingu Asanu ndi awiri....

Tsopano zindikirani. Pamene Angelo asanu ndi awiri anabwera kudzawomba Malipenga awo, apo panali bingu limodzi. Pamene lsraeli anasonkhanitsidwa, panali lipenga. Pamene sipadzakhalanso nthawi,“ lipenga lotsiriza, bingu limodzi. Koma apa pali Mabingu Asanu ndi awiri olunjika, kumene mu mzere: wanu, thuwu, firii, folo, faifi, sikisi, seveni, ndiyo nambala yangwiro. Mabingu Asanu ndi awiri mu mzere, analankhula, osati.kupanga basi-basi wani, thuwu, firii, folo, faifi, sikisi, seveni, molunjika. [M'bale Branham anagogoda pa guwa kasanu ndi kawiri- Mkonzi.] Ndiye, Miyamba siyikanakhoza kulemba lcho. Miyamba siyikanakhoza kudziwa za lcho, palibe chirichonse, chifukwa apo palibe kanthu kuti kazipitirira. lyo inali nthawi ya kumasuka. lcho chinali chachikulu chotero, mpaka, lcho chinasungidwa chinsinsi kwa Angelo.

Tsopano, chifukwa? Ngati satana akanachigwira lcho, iye mwina akanachita kuwononga kwakukulu. Apo pali chinthu chimodzi chomwe iye sakuchidziwa. Tsopano, iye akhoza kumasulira chirichonse chimene iye akufuna kutero, ndi kukopera mphatso ya mtundu uliwonse, (ine ndikuyembekeza inu mukuphunzira), koma iye sangakhoze kudziwa lchi. lcho sichinalembedwe nkomwe mu Mawu. lcho chiri chinsinsi kwathunthu. Angelo, chirichonse, kutseka pakamwa. Ngati iwo akanapanga kusuntha kumodzi, icho mwina chikanapereketsa chinachake, kotero iwo iwo anangotseka pakamwa, kusiya kuyimba azeze. Chirichonse chinayima.

Zisanu ndi ziwiri, nambala yangwiro ya Mulungu. Zisanu ndi ziwiri, basi mpaka mmusi mwa mzere. Mabingu Asanu ndi awiri analankhula molunjika pamodzi, monga iwo anali kutchula chinachake. Zindikirani, pa nthawi imeneyo, Yohane anayamba kulemba lcho. lye anati, “usati ulembe lcho.” Yesu sanalankhule konse za lcho. Yohane sakanakhoza kulemba lcho. Angelo sadziwa kanthu za lcho. Nchiyani lcho? Ndicho chinthu chimene, Yesu anati, “Ngakhale Angelo a Kumwamba sankadziwa” kanthu za lcho. Mukuwona lye sanachidziwe lcho, lye mwini. Anati, “Mulungu yekha” angachidziwe lcho. Koma lye anatiwuza ife, “pamene ife tidzayamba kuwona zizindikiro izi zikubwerapo.” Tsopano inu mukufika kwinakwake? Chabwino. Zindikirani, ife tikuyamba kuwona zizindikiro izi zikubwerapo. Mukuwona? Ngati satana akanachigwira lcho.

Ngati inu mukufuna chinachake kuti chichitike.Tsopano inu mudzayenera kutenga mawu anga kwa izi. Ngati inu mukukonzekera kuchita chinachake, ine ndikudziwa bwino kuposa kuwuza aliyense za icho. Osati kuti munthu ameneyo adzachinena icho, koma satana adzachimva icho. Mukuwona? lye sangakhoze kuchipeza icho, mu mtima wanga umo, malingana ngati Mulungu wachitsekera icho ndi Mzimu Woyera, kotero chiri pakati pa ine ndi Mulungu. Mukuwona? lye sakudziwa kanthu za icho mpaka inu mutachilankhula icho, ndiye iye amachimva icho. Ndipo ine ndayesera.ine ndimawawuza anthu ine ndidzachita chinthu chakuti-chakuti, ndipo yang'anani Mdierekezi amadula gudumu lirilonse limene iye angakhoze, kuti akafike kumeneko, mwawona, kuti andipambane ine kwa icho. Koma ngati ine ndipeza vumbulutso kuchokera kwa Mulungu, ndipo nkusangonena kanthu za ilo, ndiye icho nchosiyana.

Kumbukirani, satana adzayesa kukopera. lye adzayesa kukopera chirichonse chimene Mpingo uti udzachite. lye wayesera kuchita izo. lfe tikuzindikira izo, kupyolera mu wotsutsakhristu. Koma ichi chiri chinthu chimodzi chimene iye sangakhoze kukopera. Apo sipadzakhala kutsanzira kwa ichi, mwawona, chifukwa iye sakuchidziwa lcho. Palibe njira kuti iye adziwe lcho. lcho chiri chikoka chachitatu. lye basi sakudziwa kanthu za lcho. Mukuwona. lye sakuchimvetsa lcho.

Koma apo pali chinsinsi chikugona pansi pa lcho! ulemerero kwa Mulungu wa Mmwambamwamba! lne sindingakhoze konse kuganiza mofanana, moyo wanga wonse. Pamene ine ndinawona.... Tsopano, ine sindikudziwa chomwe.ine ndikudziwa sitepe yotsatira pamenepo, koma ine sindikudziwa chomwe, momwe ndingamasulire icho. Sizikhala motalika. lne ndalemba apa, pamene icho chinachitika, ngati inu mungakhoze kuwona apa, “Yima. usapite patali kuposa izi pomwe apa.”

lne sindiri woyandikira kuti ndikhale wotentheka. lne ndikungonena chowonadi. Koma inu mukukumbukira, nsapato yaying'ono, yomwe ine nthawizonse ndayesera kufotokoza momwe kuti moyo unkagona pafupi ndi chakuti ndi chakuti, ndi chikumbumtima cha mkati, ndi zinthu za mtundu umenewo? Chomwe, chinangopanga gulu lalikulu la zokopera kuyambikira pa icho. Momwe iwo ayenera kulinyamula dzanja, ndi kuwagwira anthu, ndi kukhala ndi manjenje? Aliyense anali nako kunjenjemera mu manja awo? Koma inu kumbukirani, pamene lye ananditengera ine pamwamba apo, ndi kunena, “lchi ndi chikoka chachitatu chija, ndipo palibe mmodzi adzachidziwe lcho.” lnu mukukumbukira izo? Masomphenya samalephera konse. lwo ali mwangwiro chowonadi.

Tsopano zindikirani. Kumbukirani masomphenya a kuwundana? (Charlie, apa inu muli.) China chake chikuchitika, ine ndinakuwuzani inu, sabata ino, kuti inu.lzo zakhala zonse pozungulira inu, koma ine ndikudabwa ngati inu munazindikira izo. Kumbukirani kuwundana, kwa masomphenya a Angelo, pamene ine ndinachoka kuno kuti ndipite ku Arizona? lnu mukukumbukira Ndi Nthawi Yanji Ino, Ma bwana? lnu mukukumbukira izo? Zindikirani, apa panali kuphulika kumodzi kokha kwa bingu, ndipo Angelo asanu ndi awiri anawonekera. Nkulondola uko? Kuphulika kumodzi kwa bingu, Angelo asanu ndi awiri anawonekera. Ndipo ine ndinawona Mwana wa nkhosa pamene iye anali atatsegula chisindikizo choyamba, ndipo ine ndinamva, ngati ilo linali liwu la bingu, ndipo chimodzi cha zamoyo zinayi chinati, Bwera ndipo dzawone. Zindikirani, bingu limodzi, Mauthenga Asanu ndi awiri omwe asindikizidwa ndipo sangakhoze kuwululidwa mpaka tsiku lotsiriza, la m'badwo uno. Mukuwona chimene ine ndikutanthawuza?

Tsopano, kodi inu mwalizindikira gawo lachinsinsi la sabata yino? Ndicho chomwe lcho chiri. Ndicho chomwe lcho chakhala chiri. lcho chakhala chisali munthu wokhalapo, m-mwamuna. lcho chakhala chiri Angelo a Ambuye. Zindikirani. Pali mboni, za atatu, akhala mkati muno, kuti sabata yapitayo, kupitirira pang'ono sabata yapitayo, ine ndinali pamwamba, kutali uko mu mapiri, pafupifupi ndi ku Mexico, ndi abale awiri omwe akhala apa. Ndikutola chisoso, kapena zomamatira, kuchokera pa mwendo wa thrauza yanga; ndipo kuphulika kunachitika, komwe pafupifupi, kunawoneka ngati, kunagwedezera mapiri pansi. Tsopano, uko nkulondola. lne sindinawawuze konse abale anga, koma iwo anazindikira kusiyana kwake. Ndipo lye ananena kwa ine, “Tsopano konzekera. Pita kummawa.”

Apa pali kumasulira kwa masomphenya aja. Mukuwona? Tsopano, kuti ndikudziwitseni inu, M'bale Sothmann sanayipeze nyama yomwe iye anapitira. lfe tinali kuyesera kumupezera iyo iye. Ndipo lye anati, “Tsopano, usiku uno, mwa chizindikiro kwa iwe, iye sachita izo. lwe uyenera kudzipatulira wekha pa nthawi yino kukuchezera kwa Angelo awa.” Ndipo ine ndinamverera ngati ndasokonezeka, inu mukukumbukira. Ndipo ine ndinali kumadzulo. Angelo anali kubwera kummawa. Ndipo pamene lwo anali kubwera apo, ine ndinanyamulidwa nawo lwo, (inu mukukumbukira izo?) akubwera kummawa.

-----
Ndipo kodi inu munazindikira? Mngelo mmodzi uja, “ine ndinati, mkati umo, munali Mngelo wachirendo.” lye ankawoneka mochuluka kwa ine kuposa aliyense wa lwo. lnu mukukumbukira izo. lwo anali mu kuwundana; atatu pa mbali, ndipo mmodzi pamwamba. Ndipo mmodzi woyandikira kumene kwa ine apa, kuwerenga kuchokera kumamzere kupita kumanja, akanakhala Mngelo wachisanu ndi chiwiri. lye anali wowalirapo, anatanthawuza mochuluka kwa ine kuposa onse a lwo. lnu mukukumbukira? lne ndinati, lye anali atatulutsa chidali chake, monga chonchi, ndipo anali kuwulukira chakummawa (inu mukukumbukira) monga chonchi. lne ndinati, “lye anandinyamula ine mmwamba; kundikwezera ine mmwamba.” Kodi mukukumbukira icho?

Apa lcho chiri, yemwe ali nacho chisindikizo chachisanu ndi chiwiri, chinthu chimene ine ndachidabwa moyo wanga wonse. Ameni! Zisindikizo zina izo zinatanthawuza zochuluka kwa ine, zedi, koma, o, inu simukudziwa chomwe lchi chatanthawuza, kwa nthawi imodzi mu moyo! lne ndinapemphera, ine ndinalirira kwa Mulungu. Utatha msonkhano uja wa ku Phoenix, anthu ali wonse ali ndi ine akudziwa. lne ndinagona mu mapiri. Mmawa umodzi, ine ndinawuka ndipo ndinapita mmwamba mu Sabino Canyon, mapiri akulu, akale, aatali awo. Ndipo ine ndinapita pamwamba mmenemo. Ndipo uko kuli kanjira-kamapazi kakang'ono, iwe utatha kuyamba, kupita pamwamba ku Phiri la Lemmon, komwe kuli kuyenda kwa mailosi makumi atatu, pafupifupi chisanu cha mapazi makumi atatu pamwamba apo.

Kotero, pamwamba mu phiri, mmawa kwenikweni kusanache, ndikupita pamwamba kupyola mu kanjira-kamapazi kakang'ono aka, ndikugudubuza miyala potsatira. lne ndinamverera kutsogozedwa kuti nditembenukire ku njira iyi. Ndipo ine ndinapotoloka, ndi kupita mmwamba mu miyala yina yayikulu, yosongoka, o, mai, mazana a mapazi mmwamba. Ndipo ine ndinagwada pansi pakati pa miyala imeneyo. lne ndinagoneka pansi Baibulo ili, ndi kugoneka pansi bukhu ili... bukhu la zolemba laling'ono ili. lne ndinati, “Ambuye Mulungu, masomphenya awa akutanthawuza chiyani?” lne ndinati, “Ambuye, iwo... Kodi iwo akutanthawuza kufa kwanga?” lnu mukukumbukira, ine ndinakuwuzani inu, lne ndinkaganiza iwo akanatanthawuza imfa yanga, chifukwa chinachake chinaphulika mpaka chinangondigwedezera ine ku zidutswa.” lnu mukukumbukira. Ndi angati akudziwa.... anamvapo izo? Zedi, mwawona, nonse a inu. Ndipo ine ndinakganiza iyo ikanakhoza kutanthawuza imfa yanga.

Ndiyeno mu chipinda, ine ndinati, “Chinali chiyani iwo, Ambuye. Chikutanthauza chiyani? Kodi iwo akutanthawuza kuti ine ndikukafa? Ngati izo ziri, chabwino, ine sindiriwuza banja langa. lngondirolani ine ndizipita, mwawona, ngati ntchito yanga yatha.” Ndipo ine ndinati. “Tsopano, chinali chiyani icho? Koma lye anatumizanso umboni, inu mukukumbukira ine ndikukuwuzani inu, kuti izo zinali iyo? ko kunali kupitiriza kwa ntchito yanga.”

O! lnu mukumva izo, mukuwona? Ndipo nditakhala pamwamba mu Sabino Canyon. Atate Akumwamba akudziwa ichi. Mowona basi monga inu mukuwona izo zikufika pochitika, Angelo amenewo kubwera mpaka mmusi ndi kutsimikizira uthenga uliwonse kuti uli momwemo. Ndiye, inu mukudziwa ngati lwo ukuchokera kwa Mulungu, kapena ayi. lzo zinaloseredwa, inu, mwa masomphenya. lne sindikanakhoza kukuwuzani inu mpaka misonkhano itatha, chifukwa ine ndinaletsedwa kutero.

Mu Sabino Canyon, nditakhala pamwamba apo mmawa uja, ine ndinali nditakweza manja anga mmwamba. Ndipo changa. Mphepo inali itakupizira pansi chipewa changa chakuda chakale. Pamene.ine ndinali kuyimirira pamenepo, ndi manja anga mmwamba, ndikupemphera. lne ndinati, “Ambuye Mulungu, ichi chikutanthawuza chiyani? lne sindingakhoze kumvetsa izo, Ambuye. Kodi ine ndizichita chiyani? Ngati ili nthawi yanga yopitira Kwathu, ndiroleni ine ndipitire pamwamba pano, ndi pamene iwo sadzandipeza konse ine. lne sindikufuna aliyense kumadzabuma pozungulira, ngati ine ndikupita. lne ndikufuna basi banja kuti liganize kuti ine ndinangokayenda. Ndipo iwo sadzandipeza ine. Ndibiseni ine penapake. Ngati ine nditi ndipite, bwanji, ndiroleni ine ndipite. Mwinamwake Joseph adzalipeza Baibulo langa litagona apa, tsiku lina, ndipo muloleni iye adzaligwiritse llo ntchito. Mwawona, ngati ine ndikuchokapo, ndiroleni ine ndipite, Ambuye.”

Ndipo ine ndinali ndi manja anga mmwamba. Ndipo, zonse mwadzidzidzi, chinachake chinagunda dzanja langa. lne sindikudziwa. lne sindingakhoze kunena. Kodi ine ndinali nditagona? lne sindikudziwa. Kodi ine ndinkayenda ndiri mtulo? lne sindikudziwa. Kodi anali masomphenya? lne sindingakhoze kukuwuzani inu. Chinthu chokha ine ndingakhoze kunena chiri chomwe ine. Chinthu chomwecho basi momwe Angelo awo analiri! Ndipo icho chinakhuza dzanja langa. Ndipo ine ndinapenya, ndipo ilo linali lupanga. Ndipo ilo linali ndi chikumbu cha ngale, chokongola kwenikweni; ndipo chinali ndi chotetezera pa ilo, chiri ndi golide. Ndipo mpeniwo unkawoneka monga chinachake monga koromu monga siliva, kokha unali wowala kwenikweni. Ndipo iwo unali wa mbali zakuthwa mowopsya, o, mai! Ndipo ine ndinaganiza, “Sichiri icho chinthu chokongoletsa!” Langokwanira dzanja langa! lne ndinaganiza, Ndicho chokongola kopitirira. Koma,” ine ndinati, “heyi, ine nthawizonse ndimawopa zinthu zimenezo”, lupanga. lne ndinaganiza, “lne ndichita nalo chiyani ilo?”

Ndipo basi pomwepo Liwu linagwedezera pansi kupyola pamenepo, lomwe linaswa miyala. Linati, “Ndilo Lupanga la Amfumu!” Ndiyeno ine ndinatuluka mwa izo. Lupanga la Amfumu.” Tsopano, ngati llo likanati, Lupanga la mfumu.“ Koma llo linati, “Lupanga la Amfumu.” Ndipo pali mmodzi yekha “Amfumu”, ndipo ndiye Mulungu. Ndipo lye ali nalo Lupanga limodzi, ndilo Mawu Ake, womwe ine ndakhala nawo moyo. llo, kotero ndithandizeni ine, Mulungu; ndikuyimirira pa gome Lake Loyera apa, ndi Mawu awa oyera atagona apa! llo liri Mawu! Ameni!

O, ndi tsiku lanji lomwe ife tikukhalamo! Ndi chinthu chachikulu bwanji! Mukuwona chinsinsi ndi chobisika? Chachitatu. Nditayima pamenepo pamene ichi chinandichokera ine, Chinachake chinangobwera kwa ine ndipo chimati, “usati uwope”. Tsopano, ine sindinamve liwu lirilonse. Monga mkati mwa ine, munalankhula. lne ndikungoyenera kukuwuzani inu chowonadi, chimodzimodzi basi chomwe chinachitika. Chinachake chinagunda, ndipo chinati, “Usati uwope. lchi ndi chikoka chachitatu chija.”

Chikoka chachitatu! lnu mukuchikumbukira lcho? lye anati, “lwe wakhala nazo zokopera zambiri pa ichi, zomwe iwe umayesera kufotokoza. Koma,” anati, “usati ngakhale uyesere, lchi.” lnu mukukumbukira izo? Ndi angati akukumbukira masomphenya aja? Bwanji, ndi ponseponse. lzo zinajambulidwa, ndipo kulikonse. lzo zakhala pafupi zaka zisanu ndi chimodzi zapitazo, zisanu ndi ziwiri zapitazo. Zakhala zaka zisanu ndi ziwiri zapitazo. Anati, “usati uyesere kufotokoza lcho.” Anati, “lchi ndi chikoka chachitatu, koma lne ndidzakakomana nawe iwe mkati umo.” Nkulondola uko? lye anati, “Usati uyesere....”

lne ndinali kuyima ndi n-nsapato ya mwana wamng'ono, pamene lye anandiwuza ine. Anati, “Tsopano panga chikoka choyamba chako. Ndipo pamene iwe utero, nsomba idzathamangira nyambo.” Anati, “Ndiye uyang'anire chikoka chachiwiri chako,” anati, “chifukwa lcho chidzangokhala kansomba kakang'ono.” lye anati, “Ndiye chikoka chachitatu chidzayigwira iyo.” Ndipo azitumiki onse awo anandizungulira ine, anati, “M'bale Branham, ife tikudziwa inu mukhoza kuchita izo! Aleluya! M'bale Branham!” Ndipo pamene ine nthawizonse ndimazingirira, ndi gulu la azitumiki. Mukuwona? lne ndimakonda anthu. lwo amafuna kuti iwe ufotokoze chirichonse, ichi, icho.

Ndipo ine ndinati, “Chabwino, lne ndinati, lne sindikudziwa.” lne ndinati, “lne ndamvetsa kupha kwa nsomba. Tsopano, ine ndinati, tsopano, chinthu choyamba iwe umachita. Apa ndi momwe zimachitidwa. lwe umawona nsomba zonse pozungulira; iwe uyenera kugwedeza nyambo.” Chabwino, ndizo chimodzimodzi machenjerero owedzera nsomba. Kotero ine ndinati, “gwedezani nyambo”. Tsopano, inu mukuwona, pamene ine ndinagwedeza nyambo, nthawi yoyamba, tsopano nsomba imatsatira iyo. Koma iwo anali aang'ono. Ndipo ndimo monga momwe iwo anali kuphera. Kotero ndiye ine ndinati, “Ndiye inu mudza- inu mudzayika.” Ndipo ine ndinayigwedeza nkuyitulutsa iyo, pa gombe. Ndipo ine ndinali ndi nsomba, koma iyo inkawoneka ngati kakhungu pa nyambo, iyo inali chabe... iyo inali yaying'ono kwambiri. Ndiyeno ine ndinali kuyimirira pamenepo, ndipo chinachake chinati, “lne ndinakuwuza iwe kuti usachite izo!” lne ndinayamba kulira.

Chingwe chonse chinali chitamangana mondizungulira ine, monga chonchi. Ndipo ine ndinali... ndinali nditayima pamenepo, ndikulira, ndi mutu wanga pansi monga choncho. lne ndinati, “Mulungu! O, ine... Ndikhululukireni ine! lne- munthu wopusa. ndinali... ndinali kuyimirira apo, ndikulira, mutu wanga pansi monga chonchi. lne ndinati, “Mulungu! O, ine... Mundikhululukire ine! lne- ine ndine munthu wopusa. Ambuye, musati. Mundikhululukire ine.” Ndipo ine ndinali nacho chingwe ichi. Ndipo icho, chimene ine ndinali nacho mu dzanja langa, inali nsapato ya mwana wamng'ono, pafupi yotalika chonchi. Ndipo ine ndinali nacho chingwe icho, chinali pafupi monga kunenepa kuzungulira chala changa, pafupi theka la inchesi, ngati. Ndipo kachibowo mu nsapato iyi kanali chabe pafupi usinkhu wa... locheperapo kuposa w- wani sikisitinifi, mwinamwake, ya inchesi, mu kachibowo. Ndipo ine ndinali kuyesera kuyimanga nsapato yaying'ono iyi, ndi chingwe cha inchesi yayikulu ichi. Ndipo liwu linabwera, linati, “lwe sungakhoze kuwaphunzitsa makanda Achipentekoste zinthu zauzimu.” Anati, “Tsopano, asiye iwo okha!”

Ndipo basi ndiye lye anandinyamulira ine mmwamba. lye ananditengera ine mmwamba, ndi kundikhazika ine pamwamba kwambiri patali, kumene msonkhano unali kuchitika. Amawoneka ngati chihema kapena kachisi, wa mtundu wina. Ndipo ine ndinapenya, ndipo apo panali kabokosi kakang'ono, monga, malo aang'ono mkati mwake.

Ndipo ine ndinawona Kuwala uko kunali kulankhula kwa wina wake, pamwamba pa ine, Kuwala kuja kumene inu mumakuwona pa chithunzi apo. lko kunazungulira kuchoka kwa ine, monga chonchi, ndipo kunapita pamwamba pa chihema icho. Ndipo anati, “lne ndikakumana nawe iwe m'menemo.” Ndipo anati, “Ichi chidzakhala chikoka chachitatu, ndipo iwe suzauza wina ali yense!” Ndipo mu Sabino Canyon, Iye anati, “Ichi ndi chikoka chachitatu,” Ndipo pali zinthu zitatu zazikulu zomwe zikupita nacho lcho. Ndipo chimodzi chafutukulidwa lero... kapena dzulo; chimodzi chinacho chafutukulidwa lero; ndipo pali chinthu chimodzi chimene ine sindingakhoze kumasulira, chifukwa icho chiri mu chilankhulo chosadziwika. Koma ine ndinayima pomwepo ndi kuyang'ana molunjika kumene pa lcho. Ndipo ichi chiri chikoka chachitatu chikubwera. Ndipo Mzimu Woyera wa Mulungu... O, maine! Ndicho chifukwa kumwamba konse kunali chete!

Werengani akaunti yonse mu...
Chisindikizo Chachisanu ndi Chiwiri.


Chinsinsi cha Khristu.

Chingerezi Kalatayi
webusaiti.

Buku la
Chivumbulutso.

Mulungu ndi Sayansi
Index. - Archaeology.

Mkwatulo ukubwera.

Nkhani yabwino. Yesu
adafera machimo ako.

Ubatizo wamadzi.

 

Mtambo wauzimu.

Lawi la Moto.

Kuyenda kwa
Chikristu.

Mulungu ndi mbiriyakale
mndandanda Index.

M'mandamo mulibe.
Iye ali wamoyo.

Wamoyo Mawu
mndandanda.

Nthawi yotsiriza
mndandanda.

Mibadwo isanu ndi
iwiri ya mpingo.

Mndandanda wathu wa
uthenga.

Chingalawa cha Nowa.

Zisindikizo Zisanu
ndi ziwiri.

Dzina la Mulungu.

Tchimo loyambirira.
Kodi awa anali apulo?

Archaeology.
Sodomu ndi Gomora.

Mndandanda
Khrisimasi.

  Lemba linena...

Kenaka ndinaona mngelo wina wamphamvu akutsika kuchokera kumwamba. Anavala mtambo ndipo anali ndi utawaleza pamutu pake. Nkhope yake inali ngati dzuwa, ndipo miyendo yake inali ngati mizati yamoto.

M’dzanja lake munali kabuku kakang’ono kotsekulidwa. Phazi lake lamanja linaponda m’nyanja ndipo phazi lake lamanzere linaponda pa mtunda.

Mngeloyo anafuwula kwambiri ngati kubangula kwa mkango. Atangofuwula, kunamveka kugunda kwa mabingu asanu ndi awiri.

Chivumbulutso 10:1-3


Dinani pa chithunzi tsitsani chachikulu chithunzi kapena PDF.


Mbiri ya moyo wanga.

(PDF)

Momwe ngelo anadzera
kwa ine olalikidwa ndi.

(PDF)

Kodi ichi ndi
chizindikiro cha
mapeto, Bwana?
(PDF)
Komwe mtambo
udawonekera.

Chapter 11
The Cloud

(PDF Chingerezi)

Chapter 14
- Sabino Canyon

(PDF Chingerezi)

Chapter 9
- The Third Pull

(PDF Chingerezi)

Ndicho chimene
chinsinsi chiri,
chagona kuseri kwa
Mabingu Asanu ndi
awiri otsatana awo
akulindimuka.



Uthenga Hub... Sankhani chilankhulo chanu ndikutsitsa mauthenga aulere ochokera kwa M'bale Branham.