Chisindikizo Chachisanu ndi Chimodzi.

<< m'mbuyomu

lotsatira >>

  Mndandanda Zisindikizo-Zisanu ndi ziwiri.

Chisindikizo chachiweruzo cha Mawu.


William Branham.

Werengani akaunti yonse mu...
Chisindikizo Chachisanu ndi Chimodzi.

Chivumbulutso 6:12-14,
12 And I beheld when he had opened the sixth seal, and, lo, there was a great earthquake; and the sun became black as sackcloth of hair, and the moon became as blood;
13 And the stars of heaven fell unto the earth, even as a fig tree casteth her untimely figs, when she is shaken of a mighty wind.
14 And the heaven departed as a scroll when it is rolled together; and every mountain and island were moved out of their places.

Tsopano ine ndikufuna inu mugwirize Bukhu lanu monga chonchi, Mateyu 24 ndi Chivumbulutso 6, monga chonchi. [M'bale Branham wagwirizira Baibulo lake lotsegulidwa pa mitu iwiri iyi- Mkonzi.] Ndipo tiyeni tifanizitse chinachake apa chabe pang'ono pokha. Tsopano, yang'anani ichi tsopano, ndipo inu mukhoza kuzipeza chabe momwe-momwe izo ziliri. Mwawona, chimene Mwanawankhosa apa akusonyeza, chimodzimodzi mu chophiphiritsa, chimene Iye ananena cha apa mu Mawu. Kuchita chimodzimodzi, kotero kuti zikupanga icho kulondola. Tsopano, ndicho chonse chiri kwa icho. Apa pali. Apa pali mmodzi, Iye akulankhula za icho, ndipo apa pali pamene icho chinachitika. Mukuwona? Icho chiri chabe kutsimikizira kwangwiro. Tsopano, tiyeni tiyang'ane pa mutu wa 24 wa Mateyu Woyera, ndi Chivumbulutso 6, ndi kufanizitsa mutu wa 24 wa Mateyu. Ife tonse tikudziwa kuti umenewo unali mutu umene sikolala aliyense, munthu aliyense amapitapo, kukalankhula za nthawi ya Chisawutso. Izo zimachokera pa mutu wa 24 wa Mateyu.

Ngati izo ziri choncho, tsopano... Pakuti ife tikudziwa kuti Chisindikizo Chachisanu ndi chimodzi ichi chiri Chisindikizo chachiweruzo. Chiri Chisindikizo chachiweruzo, momwemo chomwe Icho chiri. Tsopano, onani, ife takhala nako-kukwera kwa wotsutsakhristu. Tawuwona Mpingo ukupita; tsopano Iwo watsirizika, ukupita mmwamba. Ndiye ife tikuwawona ofera, a iwo Ayuda kumbuyo uko, pansi pa guwa. Tsopano apa pali kumatulidwa kwa chiweruzo, pa anthu amene ali. Kuchokera mu chiweruzo cha Chisawutso ichi mudzatuluka zikwi zana limodzi makumi anayi ndi zinayi Ayuda owomboledwa. Ine nditsimikizira kwa inu kuti iwo ali Ayuda, ndipo osati Amitundu. Iwo alibe chochita naye Mkwatibwi, osati kanthu. Mkwatibwi, ife tamuwona kale Mkwatibwi wapita. Inu simungachiyike icho pena paliponse; osabwereranso mpaka mutu wa 19 wa Bukhu la Chivumbulutso.

Tsopano zindikirani, pakuti, Chisindikizo Chachisanu ndi chimodzi chiri Chisindikizo chachiweruzo cha Mawu. Tsopano, apa, tiyeni tiyambe tsopano ndipo tiyeni tiwerenge Mateyu Woyera, mutu wa 24. Tsopano ine ndikungofuna kukupatsani inu chinachake apa ndangoziyang'ana, kuti ndipeze. Tsopano, Mateyu Woyera, kuchokera 1 mpaka 3, chabwino, ndi pamene ife titi tiwerenge poyamba.
Ndipo Yesu anatuluka, ndipo anachoka ku kachisi: ndipo akuphunzira ake anadza kwa iye kuti adzamuwonetse iye kamangidwe ka kachisiyo.
Ndipo iye anati kwa iwo, Musawone inu zinthu zonse izi? indetu Ine ndinena kwa inu, Sipadzakhala umodzi kukhala utasiyidwa apa mwala umodzi pamwamba pa umzache, umene sudzagwetseredwa pansi.
[Tsopano] ndi [ndime ya 3] pamene iye anakhala pa phiri la Azitona, ophunzira anabwera kwa iye mwapadera, kunena, Tiwuzeni ife, pamene zinthu izi ziti zidzakhale? chidzakhala chiyani chizindikiro cha kudza kwanu, ndi cha mathero a dziko?

-----
Zindikirani, tsopano. Tsopano ife tiwerenga, poyamba, kwa.... “Ndiye Iye anawayankha iwo....” Ndiyeno Iye ayamba kuwayankha tsopano, ndipo ife tikufuna kufanizitsa izo ndi Zisindikizo. Tsopano yang'anani. Chisindikizo Choyamba chiri Chivumbulutso 6:1 ndi 2. Tsopano ife tiwerenge 6:1 ndi 2.
Ndipo-ndipo ine ndinawona.Mwanawankhosa pamene iye anali atatsegula chimodzi cha zisindikizo, ndipo ine ndinamva, ngati kuti unali mkokomo wa bingu, chimodzi cha zamoyo zinai kunena, Bwera ndipo udzawone.
Ndipo ine ndinawona, ndipo tawonani kavalo woyera: ndipo iye amene anakhala pa iye anali nawo uta; ndipo korona anapatsidwa kwa iye: ndipo iye anatulukira akugonjetsa, ndi kukagonjetsa.

Munthu ameneyu tinampeza kuti anali ndani? Wotsutsa Khristu. Mateyu 24, tsopano, 4 ndi 5:
Ndipo Yesu anayankha ndipo anati kwa iwo-kwa iwo, Samalani kuti munthu asakunyengeni inu. Pakuti ambiri adzabwera mu dzina langa, kunena, ine ndine Khristu; ndipo adzanyenga ambiri.

Mwaona izo? Wotsutsa Khristu. Apo pali Chisindikizo chanu. Mwawona. Iye wachilankhula icho apa; ndipo apa iwo akutsegula Chisindikizo, ndipo apa iye anali, mwangwiro kumene. Tsopano Chisindikizo Chachiwiri, Mateyu 24 ndi 6, Chivumbulutso 6:3 ndi 4. Tsopano yang'anani, Mateyu 24 ndi 6. Tsopano ndiroleni ine ndiwone chimene iyo ikunena.
Ndipo inu mudzamva za nkhondo ndi mbiri za nkhondo: onani kuti inu musakhale ovutika: pakuti zinthu zonse izi ziyenera kuchitika, koma chitsiriziro chisanafikebe.
Chabwino, tiyeni titenge Chisindikizo Chachiwiri, Chivumbulutso 6:3 ndi.4. Yang'anani zomwe Iye akunena tsopano.
Ndipo pamene iye anali atatsegula chisindikizo chachiwiri, ndipo ine ndinamva chamoyo chachiwiri chikunena, Bwera... udzawone.
Ndipo pamenepo panatuluka kavalo wina yemwe anali wofiira: ndipo mphamvu inapatsidwa kwa iye amene anakhala pamenepo kuti akatenge mtendere ku dziko lapansi, ndipo kuti iwo aphane mmodzi ndi mzake: ndipo apo kunapatsidwa kwa iye lupanga lalikuru.

Mwangwiro, chimodzimodzi basi! O, ine ndimakonda kupanga Lemba kudziyankha Lokha. Kodi inu simutero? Mzimu Woyera unalemba Ilo lonse, koma Iye ali wokhoza kuliwulula Ilo. Tsopano tiyeni tizindikire Chisindikizo Chachitatu. Tsopano, iyi ili njala. Tsopano, Mateyu 24:7 ndi 8. Tiyeni tipeze 7 ndi 8, mu Mateyu.
Ndipo fuko lidzawukira motsutsa fuko, ndi ufumu motsutsa ufumu: ndipo apo kudzakhala njala,... zowawitsa,... zivomezi, mu malo akuti akuti.
Zinthu zonse izi ziri chiyambi cha chisoni.

Mukuwona, inu mukubwera bwino tsopano. Tsopano, Chivumbulutso 6, mu wa 6, tsopano ife titsegula Chisindikizo Chachitatu. Icho chikupezeka mu Chivumbulutso 6:5 ndi 6.

Ndipo pamene iye anali atatsegula chisindikizo chachitatu, ine-ine ndinawona chamoyo chachitatu chikunena, Bwera ndipo udzawone. Ndipo ine ndinapenya, ndipo tawonani kavalo wakuda; ndipo iye amene anakhala pa iye anali nawo muyeso mu dzanja lake. Ndipo ine ndinamva liwu mkati mwa zamoyo zinai likunena, Muyeso.rupiya.Muyeso wa tirigu wogula rupiya, ndi miyeso itatu ya barele yogula rupiya; ndipo ona iwe usawononge mafuta ndi.... vinyo.
Njala! Mwawona, chimodzimodzi Chisindikizo chomwecho, chinthu chomwecho Yesu ananena. Chabwino. Chisindikizo Chachinai, Azowawitsa“ ndi imfa.” Zindikirani, Mateyu 24. Ife tiwerenga ndime ya 7 ndi ya 8, ine ndikukhulupirira izo ziri, pa Chisindikizo Chachinai ichi, ine ndiri nazo apa. Chabwino. Tsopano... ndinawerenga chiyani pambuyo apa? Kodi ine ndinawerenga chinachake cholakwika? Eya, ine ndachilemba icho. Eya, ife tiri apa. Tsopano ife tikupita. Tsopano ife tipite. Chabwino, bwana.

Tsopano tiyeni tiyambire apa pa ya 7, pa ichi, Chisindikizo Chachinai; ndi pa 6 ndi 7 ndi 8, pa chimodzi chinacho, pa Chivumbulutso. Tsopano tiyeni tiwone ya 7 ndi ya 8 ya Mateyu 24. Chabwino, tsopano.
Ndipo fuko lidzawukira motsutsa fuko, ndi ufumu kutsutsa ufumu: ndipo kudzakhala njala,... zowawitsa,... zivomezi, mmalo akuti akuti. Zinthu zonse izi ziri chiyambi cha chisoni.
Tsopano Chisindikizo Chachinai, monga ife tawerenga icho cha apa, chinali.... Chisindikizo Chachinai, chinali kuyambira ya 7 ndi ya 8, pa china ichi tsopano.
Ndipo pamene iye anali atatsegula chisindikizo chachinai, ndipo tawonani.chamoyo chachinai chinati, Bwera ndipo udzawone. Ndipo ine ndinapenya, ndipo tawonani kavalo wotumbululuka....

Tsopano yembekezani. Ine ndapeza izi molakwika. Eya. Eya. Tsopano miniti chabe, tsopano, 7 ndi 8, Tsopano tiyeni tiwone, Mateyu 24:7 ndi 8. Tsopano tiyeni tiwone. Ife tipeza icho. Ndicho Chachitatu, kutsegula, sichoncho? Mateyu 24:7 ndi 8. Ine ndikupepesa. Tsopano, icho chikutsegula mvula. kapena njala, chikutsegula njala. Chabwino. Tsopano, miliri ndi imfa.... Inde, bwana. Tsopano ife tikupita kwa icho, 7 ndi 8. Tsopano, icho chidzakhala Chisindikizo Chachinai. Tiyeni tiwone pamene ife tikupeza Chisindikizo Chachinai.
Ndipo pamene iye anali atatsegula Chisindikizo Chachinai-Chachinai...” Eya, ali wokwera pa kavalo wotumbululuka, Imfa, mwawona? Ndipo ine ndinapenya, ndipo tawonani kavalo wotumbululuka: ndipo iye.kavalo wotumbululuka: ndipo dzina lake amene anakhala pa iye amatchedwa Imfa, ndipo Gehena inatsatira iye. Ndipo mphamvu inapatsidwa kwa iye pa zinai-... madera a dziko lapansi, kukapha ndi lupanga, ndi njala, ndi imfa, ndiponso ndi zirombo za padziko lapansi.
Tsopano, mwawona, imeneyo inali “Imfa.”

Tsopano, Chisindikizo Chachisanu, Mateyu 24:9-13. Tiyeni tiwone ngati ndapeza ichi molondola, tsopano kachiwiri. Mukuwona?
Ndipo ndiye iwo adzakuperekani inu kuti mukazunzidwe, ndipo adzakuphani inu [ndi zimenezotu] ndipo inu adzakudani mafuko onse chifukwa cha dzina langa. Ndipo pamene.... Ndiyeno ambiri adzakuperekani ambiri adzakhumudwitsidwa, ndipo adzaperekana wina ndi mzake, ndipo adzadana wina ndi mzake. Ndipo aneneri abodza ambiri adzawuka, ndipo adzanyenga ambiri. Ndipo chifukwa kusayeruzika kudzachuluka, chikondi cha ambiri chidzazirala. Koma iye amene adzapirire mpaka kumapeto, yemweyo adzapulumutsidwa.
Tsopano, ife tiri pa Chisindikizo Chachisanu tsopano. Ndipo umenewo unali usiku watha, mwawona. “Iwo adzakuperekani inu, kuperekana wina ndi mzake,” ndi zina zotero.

Tsopano yang'anani apa pa Chisindikizo, Chachisanu ndi chimodzi, 6:9 mpaka 11. Tsopano tiyeni tipeze chimenecho, Chivumbulutso 6:9 mpaka 11.
Ndipo pamene iye anali atatsegula chisindikizo chachisanu, ine ndinawona pansi pa guwa miyoyo ya iwo amene anaphedwa chifukwa cha mawu a Mulungu, ndi chifukwa cha umboni umene iwo anagwirizira: Ndipo iwo anafuwula ndi liwu lalikulu, kunena, Mpakana liti,... Ambuye, woyera... woona, muchita inu... kuweruza ndi kubwezera magazi athu pa iwo akukhala pa dziko lapansi? Tsopano, ndipo miinjiro yoyera inapatsidwa kwa mmodzi aliyense wa iwo; ndipo kunanenedwa kwa iwo, kuti iwo apumulebe kwa kanthawi pang'ono, mpaka antchito amzawo nawonso ndi abale awo,... ayenera kuphedwa monga iwo anatero, zikhale zitakwaniritsidwa.

Tsopano, inu mukuwona, pansi pa Chisindikizo Chachisanu, ife tikupeza apa kufera. Ndipo pansi pa 24:9 cha apa, ife... mpaka 13, ife tikupeza aponso kuti iwo anali ofera. “Iwo adzakuperekani inu, ndi kukuphani inu,” ndi zina zotero. Mwawona, Chisindikizo chomwecho kutsegulidwa. Tsopano, mu Chisindikizo Chachisanu ndi chimodzi, chiri chimodzi chomwe ife tikubwerako tsopano, Mateyu 24:29 ndi 30... 24, ndipo tiyeni titenge 29 ndi 30. Apa ife tiri. Tsopano, tsopano ife titenganso, Chivumbulutso 6:12 mpaka 17. Ndizo chimodzimodzi zomwe ife tangowerenga kumene. Tsopano mverani kwa ichi, tsopano, chimene Yesu ananena mu Mateyu 24:29 ndi 30.
Chitangotha chitsautso cha matsiku amenewo [chani... ndi chitsautso cha ichi.... chitsautso chaching'ono chomwe iwo anadutsamo apa, mwaona] dzuwa lidzadetsedwa, ndipo mwezi sudzapereka kuwala kwake, ndipo nyenyezi zidzagwa kuchokera kumwamba, ndipo mphamvu za.miyamba zidzagwedezeka: Ndiyeno kudzawonekera chizindikiro cha Mwana wa munthu mmwamba: ndiyeno mitundu yonse ya pa dziko lapansi idzabuma, ndipo iwo adzamuwona Mwana wa munthu alinkudza mu mitambo ya kumwamba ndi mphamvu ndi ulemerero wawukulu.

Now, read over here in Revelation now, the sixth seal, the one we are on right now.
Ndipo.... tawonani pamene iye anali atatsegula chisindikizo chachisanu ndi chimodzi, ndipo, onani, kunali chivomezi chachikulu; ndipo dzuwa linada ngati chiguduli [mwawona] cha ubweya, ndi mwezi unakhala ngati magazi; Ndipo nyenyezi za kumwamba zinagwa pa dziko lapansi, ngakhale monga mkuyu utaya nkhuyu zake zosacha, pamene iwo... wagwedezeka ndi mphepo yamphamvu. Ndipo miyamba inachoka monga mpukutu pamene iwo ukulungidwa pamodzi; ndipo phiri lirilonse ndi chisumbu chirichonse... zinasuntha kuchoka mmalo ake. Ndipo mafumu a dziko lapansi, ndi anthu akulu, ndi anthu olemera, ndi oyang'anira akulu, ndi anthu amphamvu, ndi munthu wa mumsinga ali yense,... munthu waufulu aliyense, anadzibisa okha mu mapanga mu matanthwe a phiri; Ndipo ananena kwa mapiri ndi matanthwe, Igwani pa ife, ndipo tibiseni ife ku nkhope ya iye amene akhala pa mpandowachifumu, ndi ku mkwiyo wa Mwana wa nkhosa: Chifukwa tsiku lalikulu la mkwiyo wake lafika;... ndani ati adzakhoze kuyima?

Mwangwiro basi, bwererani mmbuyo momwe, onani chimene Yesu ananena apa tsopano mu Mateyu 24:29. Mverani. Litatha, vuto la Eichmann uyu, ndi zina zotero.
Mwamsanga chitachitika chisawutso cha masiku amenewo dzuwa lidzadetsedwa,... mwezi sudzatisudzapereka kuwala kwake,... nyenyezi zidzagwa kuchokera kumwamba,... mphamvu za... kumwamba zidzagwedezeka [Tsopano yang'anani.] Ndiyeno padzawoneka chizindikiro cha Mwana wa munthu mmwamba: ndipo iwo adzawona, ndipo iwo. ndiyeno mitundu yonse ya pa dziko lapansi idzabuma, ndipo iwo adzawona Mwana wa munthu akubwera mu mitambo ya kumwamba ndi mphamvu yayikulu ndi... ulemerero Ndipo kutumiza angelo ake, [ndi zina zotero,] ndi... liwu la lipenga ndipo adzasonkhanitsa iwo pamodzi osankhidwa ake kuchokera ku mphepo zinai, kuchokera kumapeto a mbali yina ya kumwamba mpaka kumbali yina.

Mukuwona, chimodzimodzi basi, kufanizitsa zimene Yesu ananena mu Mateyu 24, ndi chimene mvumbulutsi apa anatsegula mu Chisindikizo Chachisanu ndi chimodzi, ziri chimodzimodzi basi.... Ndipo Yesu anali kulankhula za nthawi ya Chisawutso, mwaona. Poyamba, iye anafunsa pamene zinthu izi ziti zidzakhale, pamene kachisi ati adzachotsedwepo. Iye anayankha ilo. Chinthu chotsatira iye anafunsa, pamene iti idzabwere nthawi.Apo kunabwera m'badwo wa ofera. Ndi pamene izi ziti zidzachite, pamene wotsutsakhristu akanadzawuka; ndi pamene wotsutsakhristu ati adzachotsepo kachisi.

-----
Tsopano ine ndikufuna inu muzindikire. Yesu.Tsopano, za mawa usiku, pa Ichi, Yesu anadumpha kuphunzitsa kwa Chisindikizo Chachisanu ndi chiwiri. Icho sichiri apa. Yang'anani, Iye akupitirira ndi mafanizo tsopano, zitatha izo. Ndipo Yohane anadumpha Chisindikizo Chachisanu ndi chiwiri. Chachisanu ndi chiwiri, chotsiriza, Chisindikizo Chachisanu ndi chiwiri, icho chikhala chinthu chachikulu. Icho sichinalembedwe nkomwe, mwawona. Anadumpha Chisindikizo Chachisanu ndi chiwiri; onse a iwo anatero. Ndipo mvumbulutsi, pamene Mulungu anangoti apo panali. Yohane anati, “Kunangokhala chete Kumwamba.” Yesu sananene liwu za Icho.

Zindikirani tsopano, kubwerera ku ndime ya 12, zindikirani, palibe Chamoyo. Ndiyo ndime ya 12, kuyambira pa Chisindikizo chathu, kuti tichiwone icho chitatsegulidwa. Palibe Chamoyo, chonga, Zolengedwa zamoyo, zikuyimiridwa apa, ngakhale, monga zinaliri pa Chisindikizo Chachisanu. Chifukwa? Izi zinachitika, mbali yina ya m'badwo wa Uthenga, mu nthawi ya Chisawutso.

Werengani akaunti yonse mu...
Chisindikizo Chachisanu ndi Chimodzi.


Chinsinsi cha Khristu.

Chingerezi Kalatayi
webusaiti.

Buku la
Chivumbulutso.

Mulungu ndi Sayansi
Index. - Archaeology.

Mkwatulo ukubwera.

Nkhani yabwino. Yesu
adafera machimo ako.

Ubatizo wamadzi.

 

Mtambo wauzimu.

Lawi la Moto.

Kuyenda kwa
Chikristu.

Mulungu ndi mbiriyakale
mndandanda Index.

M'mandamo mulibe.
Iye ali wamoyo.

Wamoyo Mawu
mndandanda.

Nthawi yotsiriza
mndandanda.

Mibadwo isanu ndi
iwiri ya mpingo.

Mndandanda wathu wa
uthenga.

Chingalawa cha Nowa.

Zisindikizo Zisanu
ndi ziwiri.

Dzina la Mulungu.

Tchimo loyambirira.
Kodi awa anali apulo?

Archaeology.
Sodomu ndi Gomora.

Mndandanda
Khrisimasi.

  Lemba linena...

Kenaka ndinaona mngelo wina akuwuluka mu mlengalenga ndipo anali ndi Uthenga Wabwino wamuyaya woti akalalikire kwa anthu okhala pa dziko lapansi, kwa a mtundu uliwonse, a fuko lililonse, a chiyankhulo chilichonse ndi kwa anthu onse.

Mngeloyo anayankhula mokweza mawu kuti, “Wopani Mulungu ndi kumutamanda, chifukwa nthawi yoweruza anthu yafika. Mumupembedze Iye amene analenga thambo, dziko lapansi, nyanja ndi akasupe amadzi.”

Chivumbulutso 14:6-7


Dinani pa chithunzi tsitsani chachikulu chithunzi kapena PDF.


Mbiri ya moyo wanga.

(PDF)

Momwe ngelo anadzera
kwa ine olalikidwa ndi.

(PDF)

Lawi la Moto.
- Houston 1950.

Chapter 1
-The Forerunners.

(PDF Chingerezi)

Chapter 13
- God is Light.

(PDF Chingerezi)

Chapter 9
- The Third Pull

(PDF Chingerezi)

Icho chiyenera
kumuyika Mkhristu
aliyense ku
kudzifufuza yekha,
ndi kugwira manja
ake pamaso pa
Mulungu.



Uthenga Hub... Sankhani chilankhulo chanu ndikutsitsa mauthenga aulere ochokera kwa M'bale Branham.